Yesaya 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+ 1 Akorinto 15:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 “Imfa iwe, kupambana kwako kuli kuti? Imfawe, mphamvu yako ili kuti?”+
19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+