Oweruza 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma inu munandisiya+ n’kuyamba kutumikira milungu ina.+ N’chifukwa chake sindidzakupulumutsaninso.+ Nehemiya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,
13 Koma inu munandisiya+ n’kuyamba kutumikira milungu ina.+ N’chifukwa chake sindidzakupulumutsaninso.+
18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,