-
Levitiko 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndipo nsembe yambewu yopangidwa moteremu muzibwera nayo kwa Yehova. Muziipereka kwa wansembe, ndipo iye azipita nayo paguwa lansembe.
-