Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+ Amosi 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya,*+ ya ku Dani,+ ndi ya ku Beere-seba.*+ Ndithu, anthu amenewa adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+
14 Iwo amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya,*+ ya ku Dani,+ ndi ya ku Beere-seba.*+ Ndithu, anthu amenewa adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+