Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 36:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+

  • Ezekieli 43:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Sadzaipitsanso dzina langa poika khomo lawo pafupi ndi khomo langa. Sadzaikanso felemu la khomo lawo pafupi ndi felemu la khomo langa moti pakati pa iwowo ndi ine n’kungokhala khoma lokha lotisiyanitsa.+ Iwo anaipitsa dzina langa loyera ndi zinthu zawo zonyansa zimene anali kuchita+ moti ndinawafafaniza nditakwiya.+

  • Aroma 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena