Yoweli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitunduyi inali kuchitira maere anthu anga+ ndipo inali kupereka mwana wamwamuna kuti akhale malipiro a hule.+ Inali kupereka mwana wamkazi kuti akhale malipiro a vinyo woti amwe.
3 Mitunduyi inali kuchitira maere anthu anga+ ndipo inali kupereka mwana wamwamuna kuti akhale malipiro a hule.+ Inali kupereka mwana wamkazi kuti akhale malipiro a vinyo woti amwe.