Salimo 122:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’malo ako otchingidwa ndi khoma lolimba mupitirizebe kukhala mtendere,+Anthu okhala munsanja zako apitirizebe kukhala opanda nkhawa iliyonse.+
7 M’malo ako otchingidwa ndi khoma lolimba mupitirizebe kukhala mtendere,+Anthu okhala munsanja zako apitirizebe kukhala opanda nkhawa iliyonse.+