Ezekieli 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munthu wovala zovala zansalu uja, yemwe m’chiuno mwake munali kachikwama konyamuliramo inki ndi zolembera, anabwera n’kudzanena kuti: “Ndachita monga momwe munanditumira.”+ Yona 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+
11 Tsopano munthu wovala zovala zansalu uja, yemwe m’chiuno mwake munali kachikwama konyamuliramo inki ndi zolembera, anabwera n’kudzanena kuti: “Ndachita monga momwe munanditumira.”+
9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+