Yeremiya 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+ Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.
7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+
13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.