Salimo 107:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aona mmene amautsira mphepo yamkuntho mwa kungonena mawu,+Moti nyanjayo imachita mafunde.+ Machitidwe 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma posakhalitsa, mphepo yamkuntho+ yotchedwa Yulakilo inawomba ngalawayo.