Machitidwe 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma popeza kuti mphepo yamkuntho inali kutiwomba ndi kutikankha mwamphamvu, tsiku lotsatira anthu anayamba kutaya katundu kuti ngalawa ipepukidwe.+ Machitidwe 27:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Onse atadya ndi kukhuta, anayamba kutayira tirigu m’nyanja kuti ngalawa ija ipepukidwe.+
18 Koma popeza kuti mphepo yamkuntho inali kutiwomba ndi kutikankha mwamphamvu, tsiku lotsatira anthu anayamba kutaya katundu kuti ngalawa ipepukidwe.+