Hoseya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Nthawi zonse ndikafuna kuchiritsa Isiraeli,+ zolakwa za Efuraimu ndi zoipa za Samariya+ zimaonekera.+ Iwo amachita zachinyengo+ ndipo anthu akuba amalowa m’nyumba komanso gulu la achifwamba limasakaza zinthu panja.+
7 “Nthawi zonse ndikafuna kuchiritsa Isiraeli,+ zolakwa za Efuraimu ndi zoipa za Samariya+ zimaonekera.+ Iwo amachita zachinyengo+ ndipo anthu akuba amalowa m’nyumba komanso gulu la achifwamba limasakaza zinthu panja.+