Yesaya 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+ Luka 1:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 za kutipulumutsa kwa adani athu ndiponso m’manja mwa onse odana nafe.+
25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+