Salimo 78:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu anachita zodabwitsa pamaso pa makolo awo+M’dziko la Iguputo,+ m’dera la Zowani.+ Yesaya 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+ Yeremiya 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene sadzalumbiranso kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo.’+
11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+
7 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene sadzalumbiranso kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo.’+