Salimo 105:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+ Salimo 135:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+
9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+