Yeremiya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Onse otsala a banja loipali, kulikonse kumene ndidzawabalalitsira,+ adzaona kuti ndi bwino kufa kusiyana ndi kukhala moyo,”+ watero Yehova wa makamu. Amosi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Tamverani mawu amene Yehova wanena okhudza inu+ ana Aisiraeli, mawu okhudza banja lonse limene ndinalitulutsa m’dziko la Iguputo.+ Mawuwo ndi akuti,
3 “Onse otsala a banja loipali, kulikonse kumene ndidzawabalalitsira,+ adzaona kuti ndi bwino kufa kusiyana ndi kukhala moyo,”+ watero Yehova wa makamu.
3 “Tamverani mawu amene Yehova wanena okhudza inu+ ana Aisiraeli, mawu okhudza banja lonse limene ndinalitulutsa m’dziko la Iguputo.+ Mawuwo ndi akuti,