Yesaya 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu a nyumba ya Yakobo ndimvetsereni. Ndimvetsereni inu nonse otsala a m’nyumba ya Isiraeli,+ inu amene ndinakunyamulani kuyambira pamene munabadwa, ndiponso inu amene ndinakusamalirani kuyambira pamene munatuluka m’mimba.+ Hoseya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+
3 “Inu a nyumba ya Yakobo ndimvetsereni. Ndimvetsereni inu nonse otsala a m’nyumba ya Isiraeli,+ inu amene ndinakunyamulani kuyambira pamene munabadwa, ndiponso inu amene ndinakusamalirani kuyambira pamene munatuluka m’mimba.+
4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+