Yobu 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+ Salimo 104:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha kudzudzula kwanu, madziwo anayamba kuthawa.+Atamva mabingu anu anayamba kuthamanga mopanikizika kwambiri, Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa mphepo yamkuntho kukhala bata,+Moti mafunde a panyanja amadekha.+
11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+
7 Chifukwa cha kudzudzula kwanu, madziwo anayamba kuthawa.+Atamva mabingu anu anayamba kuthamanga mopanikizika kwambiri, Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa mphepo yamkuntho kukhala bata,+Moti mafunde a panyanja amadekha.+