Genesis 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi. Genesis 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+
9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.
8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+