Genesis 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho pamene Mulungu anawononga mizinda ya m’Chigawocho, anakumbukira Abulahamu. Anatero mwa kupulumutsa Loti ku chiwonongeko pamene ankawononga mizinda imene Loti anali kukhalako.+ Ekisodo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+ 1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+ Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+
29 Choncho pamene Mulungu anawononga mizinda ya m’Chigawocho, anakumbukira Abulahamu. Anatero mwa kupulumutsa Loti ku chiwonongeko pamene ankawononga mizinda imene Loti anali kukhalako.+
24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+
19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+