Yoswa 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+ Salimo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+ Yesaya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 N’chifukwa chake anthu onse adzataya mtima, ndipo mitima ya anthu onse idzasungunuka.+
11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+
14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+