Yoswa 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake Yoswa anachita zimene Yehova anamuuza. Mahatchi awo anawapundula,+ ndipo magaleta awo anawatentha ndi moto.+ Salimo 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+
9 Pambuyo pake Yoswa anachita zimene Yehova anamuuza. Mahatchi awo anawapundula,+ ndipo magaleta awo anawatentha ndi moto.+
9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+