Salimo 107:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti iye wathyola zitseko zamkuwa,+Ndipo wadula mipiringidzo yachitsulo.+ Yesaya 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndidzakhala kutsogolo kwako+ ndipo ndidzasalaza zitunda za m’dzikolo.+ Ndidzaphwanyaphwanya zitseko zamkuwa ndipo ndidzadula mipiringidzo yachitsulo.+
2 “Ine ndidzakhala kutsogolo kwako+ ndipo ndidzasalaza zitunda za m’dzikolo.+ Ndidzaphwanyaphwanya zitseko zamkuwa ndipo ndidzadula mipiringidzo yachitsulo.+