Yesaya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! M’mapiri mukumveka phokoso la khamu la anthu, phokoso ngati la anthu ambiri.+ Tamverani! Kukumveka chisokonezo cha maufumu, cha mitundu imene yasonkhanitsidwa pamodzi.+ Yehova wa makamu akusonkhanitsira asilikali ku nkhondo.+
4 Tamverani! M’mapiri mukumveka phokoso la khamu la anthu, phokoso ngati la anthu ambiri.+ Tamverani! Kukumveka chisokonezo cha maufumu, cha mitundu imene yasonkhanitsidwa pamodzi.+ Yehova wa makamu akusonkhanitsira asilikali ku nkhondo.+