Yeremiya 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+ Yeremiya 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+
15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+
3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+