Salimo 83:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Adani anu akuchita phokoso.+Anthu odana nanu kwambiri atukula mitu yawo.+