Oweruza 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho, Amidiyani+ anagonjetsedwa ndi ana a Isiraeli, ndipo Amidiyani sanakwezenso mutu wawo. Zitatero, dziko linakhala pa mtendere zaka 40 m’masiku a Gidiyoni.+ Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
28 Choncho, Amidiyani+ anagonjetsedwa ndi ana a Isiraeli, ndipo Amidiyani sanakwezenso mutu wawo. Zitatero, dziko linakhala pa mtendere zaka 40 m’masiku a Gidiyoni.+
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+