Yesaya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+
20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+