Yeremiya 50:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa komanso amene apulumuka m’dziko la Babulo+ kuti akanene ku Ziyoni za chilango chimene Yehova Mulungu wathu akubwezera.+ Iye akubwezera kuwonongedwa kwa kachisi wake.+ Yeremiya 51:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova.
28 “Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa komanso amene apulumuka m’dziko la Babulo+ kuti akanene ku Ziyoni za chilango chimene Yehova Mulungu wathu akubwezera.+ Iye akubwezera kuwonongedwa kwa kachisi wake.+
24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova.