Salimo 145:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo adzanena za ulemerero wa ufumu wanu.+Ndi kulankhula za mphamvu zanu,+ Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+
11 Iwo adzanena za ulemerero wa ufumu wanu.+Ndi kulankhula za mphamvu zanu,+ Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+