Yesaya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+ Mika 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+
22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+
7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+