Amosi 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.” Zekariya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo simudzakhalanso zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu okhala mu Yerusalemu, adzakhala mmenemo ali otetezeka.+
15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.”
11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo simudzakhalanso zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu okhala mu Yerusalemu, adzakhala mmenemo ali otetezeka.+