Maliro 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kumbukirani zimene zatichitikira.+ Tiyang’aneni kuti muone chitonzo chathu.+