5Mneneri Hagai+ ndi mneneri Zekariya+ mdzukulu wa Ido,+ analosera kwa Ayuda amene anali mu Yuda ndi mu Yerusalemu, m’dzina+ la Mulungu wa Isiraeli yemwe anali nawo.+
7 Pa tsiku la 24, m’mwezi wa 11 womwe ndi mwezi wa Sebati, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova anaonetsa masomphenya mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido.+ Masomphenya amene ndinaonawo ndi awa: