Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+

  • Mika 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Iye adzaimirira n’kuyamba kuweta nkhosa mu mphamvu ya Yehova+ ndiponso m’dzina lalikulu la Yehova Mulungu wake.+ Anthuwo azidzakhala kumeneko motetezeka,+ pakuti iye adzakhala wamkulu mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Hagai 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Anthu awa akunena kuti: “Nthawi yomanga nyumba ya Yehova sinakwane.”’”+

  • Hagai 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Hagai mthenga+ wa Yehova analankhula kwa anthuwo malinga ndi ntchito imene Yehova anam’patsa.+ Iye anati: “‘Ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova.”

  • Zekariya 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Uwauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “‘Bwererani kwa ine,’+ watero Yehova wa makamu, ‘ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,’+ akutero Yehova wa makamu.”’

  • Zekariya 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova wa makamu anapitiriza kulankhula kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena