Ezekieli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anautambasula pamaso panga, ndipo unalembedwa kuseri n’kuseri.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+ Chivumbulutso 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.
10 Iye anautambasula pamaso panga, ndipo unalembedwa kuseri n’kuseri.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+
5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.