Levitiko 14:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo azilamula kuti nyumbayo aigwetse pamodzi ndi miyala yake, matabwa ake ndi dothi lake lonse lomangira, ndipo zonsezi azitengere kunja kwa mzinda, kumalo odetsedwa.+ Miyambo 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Temberero la Yehova lili panyumba ya munthu woipa,+ koma malo okhala anthu olungama, iye amawadalitsa.+ Yakobo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Golide ndi siliva wanu wadyedwa ndi dzimbiri, ndipo dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani. Lidzadya mnofu wa matupi anu. Zimene mwaunjika+ m’masiku otsiriza+ zili ngati moto.+
45 Pamenepo azilamula kuti nyumbayo aigwetse pamodzi ndi miyala yake, matabwa ake ndi dothi lake lonse lomangira, ndipo zonsezi azitengere kunja kwa mzinda, kumalo odetsedwa.+
33 Temberero la Yehova lili panyumba ya munthu woipa,+ koma malo okhala anthu olungama, iye amawadalitsa.+
3 Golide ndi siliva wanu wadyedwa ndi dzimbiri, ndipo dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani. Lidzadya mnofu wa matupi anu. Zimene mwaunjika+ m’masiku otsiriza+ zili ngati moto.+