Yesaya 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinayang’anayang’ana, koma panalibe wondithandiza. Ndinayamba kudabwa, koma panalibe woti angandichirikize.+ Choncho ndinabweretsa chipulumutso ndi dzanja langa,+ ndipo ukali wanga+ ndi umene unandichirikiza. Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
5 Ndinayang’anayang’ana, koma panalibe wondithandiza. Ndinayamba kudabwa, koma panalibe woti angandichirikize.+ Choncho ndinabweretsa chipulumutso ndi dzanja langa,+ ndipo ukali wanga+ ndi umene unandichirikiza.
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+