Salimo 103:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tamandani Yehova, inu angelo+ ake amphamvu, ochita zimene wanena,+Mwa kumvera malamulo ake.+