Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthuyo anayankha kuti: “Iyayi, koma ine pokhala kalonga wa gulu lankhondo la Yehova, tsopano ndabwera.”+ Yoswa atamva mawu amenewo, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo anamuuza kuti: “Lankhulani mbuyanga kwa kapolo wanu.”

  • 2 Mafumu 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+

  • Salimo 148:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mutamandeni, inu angelo ake onse.+

      Mutamandeni, inu khamu lake lonse.+

  • Luka 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.

  • Aheberi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+

  • Chivumbulutso 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo anali kunena kuti: “Ame! Mulungu wathu wanzeru, wamphamvu+ ndi wa nyonga, atamandidwe, apatsidwe ulemerero ndi ulemu, ndipo ayamikiridwe kwamuyaya. Ame.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena