1 Mbiri 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsiku ndi tsiku anthu anali kubwera+ kwa Davide kudzamuthandiza, mpaka anachuluka n’kukhala khamu lankhondo lalikulu,+ ngati khamu lankhondo la Mulungu.+
22 Tsiku ndi tsiku anthu anali kubwera+ kwa Davide kudzamuthandiza, mpaka anachuluka n’kukhala khamu lankhondo lalikulu,+ ngati khamu lankhondo la Mulungu.+