Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+ Yoswa 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthuyo anayankha kuti: “Iyayi, koma ine pokhala kalonga wa gulu lankhondo la Yehova, tsopano ndabwera.”+ Yoswa atamva mawu amenewo, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo anamuuza kuti: “Lankhulani mbuyanga kwa kapolo wanu.”
2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+
14 Munthuyo anayankha kuti: “Iyayi, koma ine pokhala kalonga wa gulu lankhondo la Yehova, tsopano ndabwera.”+ Yoswa atamva mawu amenewo, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo anamuuza kuti: “Lankhulani mbuyanga kwa kapolo wanu.”