2 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapitanso ndi amuna+ amene anali kuyenda naye, aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala m’mizinda ya m’dera la Heburoni.
3 Davide anapitanso ndi amuna+ amene anali kuyenda naye, aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala m’mizinda ya m’dera la Heburoni.