1 Samueli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna onse amene anali kusautsidwa,+ onse amene anali ndi ngongole,+ ndi onse amene anali ndi zodandaula+ anayamba kusonkhana kwa iye,+ ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo.+ Anthu onse amene anali naye anakwana 400. 1 Samueli 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Davide pamodzi ndi amuna 600+ amene anali kuyenda naye ananyamuka ndi kupita kwa Akisi+ mfumu ya Gati, mwana wa Maoki. 1 Mbiri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.
2 Amuna onse amene anali kusautsidwa,+ onse amene anali ndi ngongole,+ ndi onse amene anali ndi zodandaula+ anayamba kusonkhana kwa iye,+ ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo.+ Anthu onse amene anali naye anakwana 400.
2 Choncho Davide pamodzi ndi amuna 600+ amene anali kuyenda naye ananyamuka ndi kupita kwa Akisi+ mfumu ya Gati, mwana wa Maoki.
12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.