2 Samueli 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Husai anapitiriza kunena kuti: “Iwe ukuwadziwa bwino bambo wako ndi amuna amene ali nawo kuti iwo ndi amphamvu+ ndipo mitima ikuwapweteka+ ngati chimbalangondo chimene chataya ana ake kuthengo.+ Ukudziwanso bwino kuti bambo wako ndi munthu wankhondo+ ndipo sangagone kumene kuli anthu. 1 Mbiri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano otsatirawa ndiwo atsogoleri a amuna amphamvu+ a Davide omwe anali kulimbikitsa nawo ufumu wake mwamphamvu pamodzi ndi Aisiraeli onse, kuti iye akhale mfumu malinga ndi mawu a Yehova+ okhudza Isiraeli.
8 Ndiyeno Husai anapitiriza kunena kuti: “Iwe ukuwadziwa bwino bambo wako ndi amuna amene ali nawo kuti iwo ndi amphamvu+ ndipo mitima ikuwapweteka+ ngati chimbalangondo chimene chataya ana ake kuthengo.+ Ukudziwanso bwino kuti bambo wako ndi munthu wankhondo+ ndipo sangagone kumene kuli anthu.
10 Tsopano otsatirawa ndiwo atsogoleri a amuna amphamvu+ a Davide omwe anali kulimbikitsa nawo ufumu wake mwamphamvu pamodzi ndi Aisiraeli onse, kuti iye akhale mfumu malinga ndi mawu a Yehova+ okhudza Isiraeli.