1 Samueli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero. 2 Samueli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Sauli atamwalira, ndiponso Davide atabwera kuchokera kokakantha Aamaleki,+ Davideyo anakhala ku Zikilaga+ masiku awiri.
6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero.
1 Sauli atamwalira, ndiponso Davide atabwera kuchokera kokakantha Aamaleki,+ Davideyo anakhala ku Zikilaga+ masiku awiri.