1 Samueli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero. 1 Samueli 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zofunkhazo kwa mabwenzi ake,+ akulu a ku Yuda, n’kunena kuti: “Landirani mphatso*+ iyi kuchokera pa zimene tafunkha kwa adani a Yehova.”
6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero.
26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zofunkhazo kwa mabwenzi ake,+ akulu a ku Yuda, n’kunena kuti: “Landirani mphatso*+ iyi kuchokera pa zimene tafunkha kwa adani a Yehova.”