2 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo ya pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide inatenga nthawi yaitali.+ Davide anapitirizabe kukhala wamphamvu+ koma nyumba ya Sauli inali kufookerafookera.+ Yobu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wolungama akuyendabe panjira yake,+Ndipo wa manja oyera+ akungowonjezeka mphamvu.+
3 Nkhondo ya pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide inatenga nthawi yaitali.+ Davide anapitirizabe kukhala wamphamvu+ koma nyumba ya Sauli inali kufookerafookera.+