Genesis 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mwamunayu sanandiuze yekha kuti, ‘Ndi mlongo wanga’? Ndipo mkaziyunso sananene yekha kuti, ‘Ndi mlongo wanga’? Zimenezitu ndachita popanda mtima wanga kunditsutsa, komanso mosadziwa kuti ndikulakwa.”+ Salimo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+ Salimo 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+
5 Kodi mwamunayu sanandiuze yekha kuti, ‘Ndi mlongo wanga’? Ndipo mkaziyunso sananene yekha kuti, ‘Ndi mlongo wanga’? Zimenezitu ndachita popanda mtima wanga kunditsutsa, komanso mosadziwa kuti ndikulakwa.”+
4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+
6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+