Salimo 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundisambitse bwinobwino ndi kuchotsa cholakwa changa,+Ndiyeretseni ku tchimo langa.+ Salimo 73:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+ Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+ Mateyu 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”
13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+
24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”